Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.09 6-7
  • Yesu Ankalemekeza Atate Wake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesu Ankalemekeza Atate Wake
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Nyamula Mtengo Wako Wozunzikirapo, ndi Kunditsatira Mosalekeza
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Muzidzichepetsa Ena Akamakuyamikirani
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Kodi Yesu Ali Ndi Makhalidwe Otani?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • ‘Mulungu Anayesa Abulahamu’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.09 6-7
Yesu anapereka ulemu kwa Atate wake

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 7-8

Yesu Ankalemekeza Atate Wake

7:15-18, 28, 29; 8:29

Yesu ankalemekeza Atate wake m’zochita komanso m’zolankhula zake. Iye ankafuna kuti anthu azidziwa kuti uthenga umene ankalalikira ndi wochokera kwa Mulungu. Choncho ankaphunzitsa zinthu zochokera m’Malemba ndipo nthawi zambiri ankakonda kugwira Malemba. Anthu akamamutamanda, iye ankakana ndipo ankawauza kuti atamande Yehova. Cholinga chake chachikulu chinali kukwaniritsa ntchito imene Yehova anamupatsa.​—Yoh. 17:4.

Kodi tingatsanzire bwanji Yesu . . .

  • tikamaphunzitsa ena Baibulo komanso tikamakamba nkhani kumisonkhano?

  • ena akamatitamanda?

  • tikamaganizira mmene tingagwiritsire ntchito nthawi yathu?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani