Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.08 7
  • Mmene Malamulo 10 Amakukhudzirani

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mmene Malamulo 10 Amakukhudzirani
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Chikondi Cha Mulungu Sichimatha
    Kodi Mungatani Kuti Mulungu Azikukondani?
  • Aisiraeli Ankafunika Kusonyeza Chikondi ndi Chilungamo
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • “Mukhale Tcheru ndi Kuyang’anira Gulu Lonse la Nkhosa”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Muzitsatira Malamulo Awiri Aakulu Kwambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.08 7
Mose waima patsogolo pa phiri la Sinai, ndipo watenga miyala iwiri yokhala ndi Malamulo 10.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 19-20

Mmene Malamulo 10 Amakukhudzirani

20:3-17

Akhristu satsatira Chilamulo cha Mose. (Akl 2:13, 14) Ndiye kodi Malamulo 10 komanso Chilamulo chonse zili ndi phindu lililonse kwa ife masiku ano?

  • Amasonyeza mmene Yehova amaonera zinthu

  • Amasonyeza zimene Yehova amayembekezera kuti tizichita

  • Amasonyeza mmene tiyenera kuchitira zinthu ndi anthu anzathu

Kodi Malamulo 10 amakuphunzitsani chiyani za Yehova?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani