Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.07 6
  • Yehova ndi Mulungu Wachilungamo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova ndi Mulungu Wachilungamo
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Abisalomu Anaukira Chifukwa cha Kunyada
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kudzikonda kwa Aminoni Kunabweretsa Mavuto
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Mumapereka Nsembe?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Muzidalira Yehova Kuti Akuthandizeni
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.07 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova ndi Mulungu Wachilungamo

Yehova sanaiwale zinthu zopanda chilungamo zimene zinachitikira Agibeoni (2Sa 21:1, 2)

Siliva ndi golide sakanathetsa mlandu wa magazi umene Sauli ndi nyumba yake anali nawo (Nu 35:31, 33; 2Sa 21:3, 4)

Anthu 7 a m’banja la Sauli anaphedwa kuti chilungamo chioneke (2Sa 21:5, 6; it-1 932 ¶1)

A Mboni za Yehova a misinkhu yosiyanasiyana, ochokera m’mayiko osiyanasiyana komanso azikhalidwe zosiyanasiyana omwe anapirira pamene ankazunzidwa komanso pamene anali m’ndende.

Kodi lemba la Aroma 12:19-21, lingatithandize bwanji ngati tachitiridwa zinthu zopanda chilungamo?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani