Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.03 22
  • Zimene Tinganene

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tinganene
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO (11 March–4 April)
  • ULENDO WOYAMBA (1-10 March, 5-30 April)
  • ULENDO WOBWEREZA
  • Zimene Tinganene
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Zimene Tinganene
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Zimene Tinganene
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.03 22
Yesu akuyambitsa mwambo wa Chakudya cha Madzulo cha Ambuye limodzi ndi atumwi ake okhulupirika.

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Zimene Tinganene

NTCHITO YOITANIRA ANTHU KU CHIKUMBUTSO (11 March–4 April)

“Ndife osangalala kukuitanirani kumwambo wofunika kwambiri womwe udzachitike padziko lonse. Mwambo umenewu ndi wokumbukira imfa ya Yesu.” M’patseni kapepala kosindikizidwa kapena ka pachipangizo chamakono. “Kapepalaka kakusonyeza nthawi komanso malo omwe mwambowu udzachitikire m’dera lathu lino. Tikukuitananinso kuti mudzamvetsere nkhani yapadera yomwe idzakambidwe kumapeto kwa mlungu woyambira March 27.”

Ngati Munthuyo Wasonyeza Chidwi: Musonyezeni [kapena mutumizireni linki ya] vidiyo yakuti Tizikumbukira Imfa ya Yesu.

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

ULENDO WOYAMBA (1-10 March, 5-30 April)

Funso: Kodi Yesu ndi ndani?

Lemba: Mt 16:16

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

ULENDO WOBWEREZA

Funso: N’chifukwa chiyani Yesu anafa?

Lemba: Mt 20:28

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira nsembe ya dipo ya Yesu?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani