Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.05 3
  • Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Yehova Anathandiza Mfumu Yehosafati
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Kodi Mumatsatira ndi Mtima Wonse Zimene Zinalembedwa?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.05 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera

Mfumu Yehosafati inachita zinthu mopanda nzeru pamene inapanga mgwirizano ndi Mfumu Ahabu (2Mb 18:1-3; w17.03-CN 24:7)

Yehova anatumiza Yehu kuti akadzudzule Yehosafati (2Mb 19:1, 2)

Yehova anakumbukira zinthu zabwino zimene Yehosafati anachita (2Mb 19:3; w15 8/15-CN 11-12:8-9)

M’bale akuyang’ana moipidwa m’bale wina amene akucheza ndi anthu ena m’malo momayeretsa Nyumba ya Ufumu.

DZIFUNSENI KUTI, ‘M’malo momangoganizira zinthu zimene abale ndi alongo anga amalakwitsa, kodi ndimaona makhalidwe awo abwino ngati mmene Yehova amachitira?’

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani