CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso ndi Moyo?”
Anthu alibe mphamvu zolepheretsa imfa kapena kubwezeretsa moyo (Yob 14:1, 2, 4, 10; w99 10/15 3 ¶1-3)
Anthu omwe anamwalira angakhalenso ndi moyo (Yob 14:7-9; w15 4/15 32 ¶1-2)
Yehova amalakalaka kudzaukitsa atumiki ake omwe anamwalira, ndipo ali ndi mphamvu zochitira zimenezi (Yob 14: 14, 15; w11 3/1 22 ¶5)
MAFUNSO OFUNIKA KUWAGANIZIRA: N’chifukwa chiyani Yehova amalakalaka kudzaukitsa atumiki ake okhulupirika? Mukaganizira zimenezi, kodi mukuona kuti Yehova ndi wotani?