April Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya April 2018 Zimene Tinganene April 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 26 Kufanana Komanso Kusiyana Komwe Kulipo Pakati pa Mwambo wa Pasika ndi Chikumbutso April 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 27-28 Kodi Tingamvere Bwanji Lamulo Lakuti, Pitani Mukaphunzitse Anthu? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kulalikira Komanso Kuphunzitsa N’kofunika Kwambiri Kuti Tipange Ophunzira April 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 1-2 “Machimo Ako Akhululukidwa” April 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 3-4 Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata April 30–May 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 5-6 Yesu Ali ndi Mphamvu Zoukitsa Anthu Amene Anamwalira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizigwiritsa Ntchito Mwaluso Zinthu Zomwe Timagwiritsa Ntchito Pophunzitsa