1 MBIRI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Kuchokera pa Adamu kufika pa Abulahamu (1-27)
Mbadwa za Abulahamu (28-37)
Aedomu ndi mafumu awo (38-54)
2
Ana 12 a Isiraeli (1, 2)
Mbadwa za Yuda (3-55)
3
4
5
6
7
Mbadwa za Isakara (1-5), za Benjamini (6-12), za Nafitali (13), za Manase (14-19), za Efuraimu (20-29), ndi za Aseri (30-40)
8
9
10
11
Aisiraeli onse anadzoza Davide kukhala mfumu (1-3)
Davide analanda mzinda wa Ziyoni (4-9)
Asilikali amphamvu a Davide (10-47)
12
13
14
15
16
Likasa linaikidwa mutenti (1-6)
Nyimbo ya Davide yothokoza (7-36)
Utumiki wa kumene kunali Likasa (37-43)
17
Davide anauzidwa kuti sadzamanga kachisi (1-6)
Pangano la ufumu ndi Davide (7-15)
Pemphero la Davide loyamika (16-27)
18
19
20
21
Davide anawerenga anthu mosavomerezeka (1-6)
Chilango chochokera kwa Yehova (7-17)
Davide anamanga guwa (18-30)
22
Davide anakonzekera zinthu zomangira kachisi (1-5)
Davide anapereka malangizo kwa Solomo (6-16)
Akalonga analamulidwa kuti athandize Solomo (17-19)
23
24
25
26
27
28
29
Zopereka zothandiza pomanga kachisi (1-9)
Pemphero la Davide (10-19)
Anthu anasangalala; ufumu wa Solomo (20-25)
Imfa ya Davide (26-30)