MLALIKI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Solomo anachita zinthu zosiyanasiyana (1-11)
Nzeru za anthu nʼzothandiza pangʼono (12-16)
Ntchito ya munthu wakhama imamubweretsera zowawa (17-23)
Idya, imwa ndipo sangalala ndi ntchito yako (24-26)
3
Chilichonse chili ndi nthawi yake (1-8)
Kusangalala ndi moyo ndi mphatso yochokera kwa Mulungu (9-15)
Mulungu amaweruza anthu onse mwachilungamo (16, 17)
Anthu ndi nyama zonse zimafa (18-22)
4
Kuponderezedwa nʼkoipa kuposa imfa (1-3)
Kuona ntchito moyenera (4-6)
Ubwino wokhala ndi mnzako (7-12)
Moyo wa wolamulira ungathe kukhala wachabechabe (13-16)
5
Uziopa Mulungu moyenera (1-7)
Aliyense ali ndi amene amamuyangʼanira (8, 9)
Mavuto amene anthu achuma amakumana nawo (10-20)
6
7
Mbiri yabwino komanso tsiku lomwalira (1-4)
Munthu wanzeru akamadzudzula (5-7)
Mapeto ndi abwino kuposa chiyambi (8-10)
Ubwino wa nzeru (11, 12)
Masiku abwino komanso masiku oipa (13-15)
Musamachite zinthu mopitirira muyezo (16-22)
Zimene wosonkhanitsa anthu anaona (23-29)
8
9
Anthu onse mapeto awo ndi ofanana (1-3)
Uzisangalala ndi moyo ngakhale kuti udzafa (4-12)
Akufa sadziwa chilichonse (5)
Ku Manda kulibe kugwira ntchito (10)
Nthawi yatsoka komanso zinthu zosayembekezereka (11)
Si nthawi zonse pamene anthu amayamikira munthu wanzeru (13-18)
10
Uchitsiru pangʼono umawononga mbiri ya munthu wanzeru (1)
Kuopsa kokhala munthu wosadalirika (2-11)
Zinthu zomvetsa chisoni zimene zimachitikira munthu wopusa (12-15)
Zinthu zopusa zimene olamulira amachita (16-20)
11
12