Akugwira ntchito pa Beteli ku Wallkill, New York
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi matenda adzathadi?
Lemba: Yes. 33:24
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi njala ingadzathedi padzikoli?
○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi njala ingadzathedi padzikoli?
Lemba: Sal. 72:16
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi n’zotheka kudzaonananso ndi achibale komanso anzathu omwe anamwalira?
○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi n’zotheka kudzaonananso ndi achibale komanso anzathu omwe anamwalira?
Lemba: Yoh. 5:28, 29
Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani tiyenera kukhulupirira kuti zimene Baibulo limanena zidzachitikadi?