August Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya August 2019 Zimene Tinganene August 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 TIMOTEYO 1-4 “Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzicheza ndi Anthu Amene Amakonda Yehova August 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | TITO 1–FILIMONI “Uike Akulu” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Achinyamata, Mukhale “Odzipereka pa Ntchito Zabwino” August 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 1-3 Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo August 26–September 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 4-6 Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Ntchito Zabwino Zimene Yehova Sangaziiwale