August 19-25
AHEBERI 1-3
Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aheberi.]
Aheb. 1:8—Yesu akulamulira ndi “ndodo yachilungamo” (w14 2/15 5 ¶8)
Aheb. 1:9—Yesu amakonda chilungamo ndipo amadana ndi kusamvera malamulo (w14 2/15 4-5 ¶7)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aheb. 1:3—Kodi Yesu wakhala akusonyeza ulemerero wofanana ndi wa Atate wake kuyambira kalekale? (it-1 1185 ¶1)
Aheb. 1:10-12—N’chifukwa chiyani mtumwi Paulo anagwiritsa ntchito lemba la Salimo 102:25-27 ponena za Yesu Khristu? (it-1 1063 ¶7)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 1:7-14 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu, kenako musonyezeni vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? koma musaonetse vidiyoyi. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 9:1-8
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 48 ndi Pemphero