CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 1-3
Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo
Yesu amakonda chilungamo ndipo amadana ndi chilichonse chomwe chinganyozetse dzina la Atate ake.
Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yesu pa nkhani yokonda chilungamo
tikamayesedwa kuti tichite chiwerewere?
wachibale wathu akachotsedwa?