Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • w24.08 102
  • Mawu kwa Owerenga

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu kwa Owerenga
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
w24.08 102

Mawu kwa Owerenga

Wokondedwa Wowerenga

M’maganiziyi muli nkhani zophunzira 5 zomwe ziyankhe mafunso otsatirawa:

  • Loyamba, kodi Yehova anakonza zotani pofuna kutithandiza kuti tizimumvera ndi kumutumikira ngakhale kuti ndife ochimwa?

  • Lachiwiri, kodi Yehova wakhala akutiphunzitsa zotani zokhudza kulapa kwenikweni, nanga wakhala akuthandiza bwanji ochimwa kuti alape?

  • Lachitatu, kodi mpingo wa ku Korinto unalangizidwa kuti uthandize bwanji munthu wina yemwe anachita tchimo lalikulu mwadala?

  • La 4, kodi akulu masiku ano angathandize bwanji munthu yemwe wachita tchimo lalikulu?

  • La 5, kodi mumpingo ungatani kuti upitirize kusonyeza chikondi ndi chifundo kwa munthu wochimwa yemwe wachotsedwa?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani