Genesis 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi ali kumeneko, Abimeleki mfumu ya Afilisiti anali kuyang’ana pawindo, ndipo anaona Isaki akucheza mwachikondi ndi mkazi wake Rabeka.+ Aefeso 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amuna inu, pitirizani kukonda akazi anu+ monga mmene Khristu anakondera mpingo n’kudzipereka yekha chifukwa cha mpingowo,+
8 Patapita nthawi ali kumeneko, Abimeleki mfumu ya Afilisiti anali kuyang’ana pawindo, ndipo anaona Isaki akucheza mwachikondi ndi mkazi wake Rabeka.+
25 Amuna inu, pitirizani kukonda akazi anu+ monga mmene Khristu anakondera mpingo n’kudzipereka yekha chifukwa cha mpingowo,+