Yeremiya 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinamwetsanso Dedani,+ Tema,+ Buza, onse odulira ndevu zawo zam’mbali,+ Ezekieli 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dedani+ unali kuchita naye malonda a nsalu zoika pazishalo za mahatchi.