Yesaya 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu: Inu amuna amtengatenga a ku Dedani oyenda pa ngamila, usiku mudzagona m’nkhalango ya m’chipululu.+ Yeremiya 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Thawani!+ Bwererani! Pitani kumalo otsika kuti mukakhale kumeneko,+ inu okhala ku Dedani!+ Pakuti Esau ndidzamugwetsera tsoka pa nthawi yomulanga.+ Ezekieli 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga.
13 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu: Inu amuna amtengatenga a ku Dedani oyenda pa ngamila, usiku mudzagona m’nkhalango ya m’chipululu.+
8 Thawani!+ Bwererani! Pitani kumalo otsika kuti mukakhale kumeneko,+ inu okhala ku Dedani!+ Pakuti Esau ndidzamugwetsera tsoka pa nthawi yomulanga.+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga.