Yesaya 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu: Inu amuna amtengatenga a ku Dedani oyenda pa ngamila, usiku mudzagona m’nkhalango ya m’chipululu.+ Yeremiya 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinamwetsanso Dedani,+ Tema,+ Buza, onse odulira ndevu zawo zam’mbali,+
13 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu: Inu amuna amtengatenga a ku Dedani oyenda pa ngamila, usiku mudzagona m’nkhalango ya m’chipululu.+