Yeremiya 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+
7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+