Genesis 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ana a Elifazi anali Temani,+ Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi.+ 1 Mbiri 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ana a Esau anali Elifazi, Reueli,+ Yeusi, Yalamu, ndi Kora.+ 1 Mbiri 1:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ana a Elifazi anali Temani,+ Omari, Zefo, Gatamu, Kenazi,+ Timina,+ ndi Amaleki.+ Ezekieli 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga. Amosi 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzatumiza moto ku Temani+ ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za ku Bozira.’+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga.