Genesis 36:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yobabi atamwalira, Husamu wa kudziko la Atemani,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+ Ezekieli 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga. Obadiya 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga.
9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+