Yeremiya 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+ Amosi 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzatumiza moto ku Temani+ ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za ku Bozira.’+ Obadiya 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+
7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+
9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+