Genesis 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ana a Elifazi anali Temani,+ Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi.+ Obadiya 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+
9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+