Genesis 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana amene Oholibama anaberekera Esau ndiwo Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Amenewa anali ana a Esau amene anabereka m’dziko la Kanani. Genesis 36:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oholibama, mkazi wake wa Esau, anaberekera Esau ana aamuna awa: Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Oholibamayu anali mwana wa Ana, komanso mdzukulu wa Zibeoni.
5 Ana amene Oholibama anaberekera Esau ndiwo Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Amenewa anali ana a Esau amene anabereka m’dziko la Kanani.
14 Oholibama, mkazi wake wa Esau, anaberekera Esau ana aamuna awa: Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Oholibamayu anali mwana wa Ana, komanso mdzukulu wa Zibeoni.