Genesis 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana amene Oholibama anaberekera Esau anali Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Amenewa anali ana a Esau amene anabereka mʼdziko la Kanani.
5 Ana amene Oholibama anaberekera Esau anali Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Amenewa anali ana a Esau amene anabereka mʼdziko la Kanani.