Genesis 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana amene Oholibama anaberekera Esau ndiwo Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Amenewa anali ana a Esau amene anabereka m’dziko la Kanani.
5 Ana amene Oholibama anaberekera Esau ndiwo Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Amenewa anali ana a Esau amene anabereka m’dziko la Kanani.