-
Genesis 36:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Oholibama, mkazi wake wa Esau, anaberekera Esau ana aamuna awa: Yeusi, Yalamu ndi Kora. Oholibamayu anali mwana wa Ana komanso mdzukulu wa Zibeoni.
-