Genesis 36:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oholibama, mkazi wake wa Esau, anaberekera Esau ana aamuna awa: Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Oholibamayu anali mwana wa Ana, komanso mdzukulu wa Zibeoni.
14 Oholibama, mkazi wake wa Esau, anaberekera Esau ana aamuna awa: Yeusi, Yalamu ndi Kora.+ Oholibamayu anali mwana wa Ana, komanso mdzukulu wa Zibeoni.