Genesis 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtsinje woyamba dzina lake ndi Pisoni, umene umazungulira dziko lonse la Havila+ kumene kuli golide. 1 Samueli 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atachoka, Sauli anapha Aamaleki+ kuyambira ku Havila+ mpaka ku Shura,+ kufupi ndi Iguputo.
11 Mtsinje woyamba dzina lake ndi Pisoni, umene umazungulira dziko lonse la Havila+ kumene kuli golide.