Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi. 1 Samueli 14:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iye anapitiriza kuchita chamuna+ ndipo anapha Aamaleki+ ndi kulanditsa Isiraeli m’manja mwa wofunkha.
19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.
48 Iye anapitiriza kuchita chamuna+ ndipo anapha Aamaleki+ ndi kulanditsa Isiraeli m’manja mwa wofunkha.