Salimo 139:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi. Mlaliki 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga momwe sudziwira mmene mzimu umagwirira ntchito m’thupi la mwana amene ali m’mimba mwa mayi ake,+ momwemonso sudziwa ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+
15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi.
5 Monga momwe sudziwira mmene mzimu umagwirira ntchito m’thupi la mwana amene ali m’mimba mwa mayi ake,+ momwemonso sudziwa ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+