Genesis 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira+ kwa Yehova Mulungu Wam’mwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi. Aheberi 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+
22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira+ kwa Yehova Mulungu Wam’mwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.
16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+