Genesis 45:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mukatenge bambo anu ndi mabanja anu n’kubwera nawo kuno kwa ine. Ndidzakupatsani zabwino za dziko la Iguputo, ndipo mudzadya zonona za dzikoli.+ Numeri 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+
18 Mukatenge bambo anu ndi mabanja anu n’kubwera nawo kuno kwa ine. Ndidzakupatsani zabwino za dziko la Iguputo, ndipo mudzadya zonona za dzikoli.+
27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+