Genesis 27:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu woona akupatse mame akumwamba,+ ndi nthaka yachonde ya dziko lapansi.+ Achulukitsenso zokolola zako ndi vinyo wako watsopano.+ Genesis 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziko la Iguputo lili m’manja mwako,+ chotero uwapatse malo abwino koposa.+ Auze akhale ku Goseni,+ ndipo ngati ukudziwapo amuna olimbikira ntchito pakati pawo,+ uwaike kukhala akapitawo oyang’anira ng’ombe zanga.”+
28 Mulungu woona akupatse mame akumwamba,+ ndi nthaka yachonde ya dziko lapansi.+ Achulukitsenso zokolola zako ndi vinyo wako watsopano.+
6 Dziko la Iguputo lili m’manja mwako,+ chotero uwapatse malo abwino koposa.+ Auze akhale ku Goseni,+ ndipo ngati ukudziwapo amuna olimbikira ntchito pakati pawo,+ uwaike kukhala akapitawo oyang’anira ng’ombe zanga.”+