Genesis 46:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+
34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+