Genesis 45:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mukatenge bambo anu ndi mabanja anu n’kubwera nawo kuno kwa ine. Ndidzakupatsani zabwino za dziko la Iguputo, ndipo mudzadya zonona za dzikoli.+ Genesis 47:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aisiraeliwo anakhazikika m’dziko la Iguputo, m’chigawo cha Goseni.+ Kumeneko anaberekana n’kuchulukana kwambiri.+
18 Mukatenge bambo anu ndi mabanja anu n’kubwera nawo kuno kwa ine. Ndidzakupatsani zabwino za dziko la Iguputo, ndipo mudzadya zonona za dzikoli.+
27 Aisiraeliwo anakhazikika m’dziko la Iguputo, m’chigawo cha Goseni.+ Kumeneko anaberekana n’kuchulukana kwambiri.+