Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 27:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma Isaki anayankha Esau kuti: “Taona, iye uja ndamuika kukhala mbuye wako.+ Ndamupatsanso abale ake onse kuti akhale atumiki ake.+ Komanso ndam’dalitsira zokolola zake ndi vinyo wake watsopano.+ Nanga chatsalanso n’chiyani choti ndikuchitire mwana wanga?”

  • Deuteronomo 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo adzakukondani ndithu, kukudalitsani,+ kukuchulukitsani+ ndi kudalitsa zipatso za mimba yanu+ ndi zipatso za nthaka yanu.+ Adzadalitsa mbewu zanu, vinyo wanu watsopano ndi mafuta anu, ana a ng’ombe zanu ndi ana a nkhosa zanu,+ m’dziko limene analumbirira makolo anu kuti adzakupatsani.+

  • 2 Mafumu 18:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 kufikira ine nditabwera kudzakutengerani kudziko lofanana ndi dziko lanulo+ kuti mukhalebe ndi moyo osafa. Ndidzakutengerani kudziko la mbewu ndi la vinyo watsopano, dziko la mkate+ ndi minda ya mpesa,+ dziko la mitengo ya maolivi a mafuta ndiponso la uchi.+ Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’+

  • Salimo 104:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+

      Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+

      Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena