Deuteronomo 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+ Yoweli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Yehova adzayankha ndi kuuza anthu ake kuti, ‘Tsopano ndikukutumizirani mbewu, vinyo watsopano ndi mafuta. Anthu inu mudzakhutadi zinthu zimenezi.+ Ine sindidzakuchititsaninso kukhala chinthu chotonzedwa pakati pa anthu a mitundu ina.+
28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+
19 Pamenepo Yehova adzayankha ndi kuuza anthu ake kuti, ‘Tsopano ndikukutumizirani mbewu, vinyo watsopano ndi mafuta. Anthu inu mudzakhutadi zinthu zimenezi.+ Ine sindidzakuchititsaninso kukhala chinthu chotonzedwa pakati pa anthu a mitundu ina.+