Deuteronomo 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma dziko limene mukuwolokerako kuti mukalitenge kukhala lanu ndi dziko lamapiri ndi zigwa.+ Ilo limamwa madzi a mvula, madzi ochokera kumwamba. Deuteronomo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo kwa Yosefe anati:+“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+
11 Koma dziko limene mukuwolokerako kuti mukalitenge kukhala lanu ndi dziko lamapiri ndi zigwa.+ Ilo limamwa madzi a mvula, madzi ochokera kumwamba.
13 Ndipo kwa Yosefe anati:+“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+