Genesis 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yosefe ndi mphukira yamtengo wobala zipatso.+ Ndithu iye ndi mphukira yamtengo wobala zipatso pakasupe.+ Iye ndi mtengo woponya nthambi zake pamwamba pa khoma* la mpanda.+
22 “Yosefe ndi mphukira yamtengo wobala zipatso.+ Ndithu iye ndi mphukira yamtengo wobala zipatso pakasupe.+ Iye ndi mtengo woponya nthambi zake pamwamba pa khoma* la mpanda.+