Deuteronomo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo kwa Yosefe anati:+“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+ Yoswa 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+
13 Ndipo kwa Yosefe anati:+“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+ Yoswa 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+
16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+