Genesis 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yosefe ndi mphukira yamtengo wobala zipatso.+ Ndithu iye ndi mphukira yamtengo wobala zipatso pakasupe.+ Iye ndi mtengo woponya nthambi zake pamwamba pa khoma* la mpanda.+ Deuteronomo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo kwa Yosefe anati:+“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+
22 “Yosefe ndi mphukira yamtengo wobala zipatso.+ Ndithu iye ndi mphukira yamtengo wobala zipatso pakasupe.+ Iye ndi mtengo woponya nthambi zake pamwamba pa khoma* la mpanda.+
13 Ndipo kwa Yosefe anati:+“Dziko lake lipitirize kudalitsidwa ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba, mame,+Ndi madzi akuya a pansi pa nthaka.+