Ekisodo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yosefe anali kale ku Iguputo.+ Anthu onse otuluka m’chiuno mwa Yakobo+ analipo 70.