Numeri 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova analankhula ndi Mose m’chipululu cha Mowabu ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano,+ kuti: Yoswa 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malire a gawo lawo kumpoto anayambira ku Yorodano, n’kupitirira kukafika kumalo otsetsereka a kumpoto kwa Yeriko,+ n’kukwera phiri chakumadzulo, n’kukathera kuchipululu cha Beti-aveni.+
35 Yehova analankhula ndi Mose m’chipululu cha Mowabu ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano,+ kuti:
12 Malire a gawo lawo kumpoto anayambira ku Yorodano, n’kupitirira kukafika kumalo otsetsereka a kumpoto kwa Yeriko,+ n’kukwera phiri chakumadzulo, n’kukathera kuchipululu cha Beti-aveni.+