Salimo 104:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu,+Mafuta amene amachititsa kuti nkhope ya munthu isalale,Ndiponso chakudya chimene chimapereka mphamvu kwa munthu.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 104:15 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 43 Nsanja ya Olonda,10/15/2011, tsa. 8
15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu,+Mafuta amene amachititsa kuti nkhope ya munthu isalale,Ndiponso chakudya chimene chimapereka mphamvu kwa munthu.*+