Genesis 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Woyamba kubadwa anali wofiira, ndipo thupi lake lonse linali ngati wavala chovala chaubweya.+ Ndiye chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Esau.*+ Genesis 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo Yakobo anayankha kuti: “Choyamba, undigulitse ukulu wako monga woyamba kubadwa.”+ Aheberi 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muonetsetsenso kuti pasakhale wadama kapena aliyense wosayamikira zinthu zopatulika, ngati Esau,+ amene anapereka udindo wake monga woyamba kubadwa pousinthanitsa ndi chakudya chodya kamodzi kokha.+
25 Woyamba kubadwa anali wofiira, ndipo thupi lake lonse linali ngati wavala chovala chaubweya.+ Ndiye chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Esau.*+
16 Muonetsetsenso kuti pasakhale wadama kapena aliyense wosayamikira zinthu zopatulika, ngati Esau,+ amene anapereka udindo wake monga woyamba kubadwa pousinthanitsa ndi chakudya chodya kamodzi kokha.+