Genesis 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yakobo anayankha Rabeka mayi ake kuti: “Koma m’bale wanga Esau ndi munthu wacheya,* pamene ine ndili ndi khungu losalala.+ 2 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa m’chiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe.” Zekariya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Zikadzatero, aneneri azidzachita manyazi pa tsiku limenelo.+ Azidzachita manyazi ndi masomphenya awo pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.
11 Pamenepo Yakobo anayankha Rabeka mayi ake kuti: “Koma m’bale wanga Esau ndi munthu wacheya,* pamene ine ndili ndi khungu losalala.+
8 Iwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa m’chiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe.”
4 “Zikadzatero, aneneri azidzachita manyazi pa tsiku limenelo.+ Azidzachita manyazi ndi masomphenya awo pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.