Genesis 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Woyamba kubadwa anali wofiira, ndipo thupi lake lonse linali ngati wavala chovala chaubweya.+ Ndiye chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Esau.*+ Genesis 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye sanamuzindikire, chifukwa manja ake anali acheya ngati manja a Esau m’bale wake. Chotero anam’dalitsa.+
25 Woyamba kubadwa anali wofiira, ndipo thupi lake lonse linali ngati wavala chovala chaubweya.+ Ndiye chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Esau.*+
23 Iye sanamuzindikire, chifukwa manja ake anali acheya ngati manja a Esau m’bale wake. Chotero anam’dalitsa.+