Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chotero Eliya anachoka kumeneko n’kupita kwa Elisa mwana wa Safati, ndipo anam’peza akulima ndi pulawo+ yokokedwa ndi ng’ombe ziwiri zamphongo. Panali mapulawo 12 oterowo ndipo pulawo yake inali kumbuyo kwa onsewo. Choncho Eliya anapita pamene panali Elisa n’kumuponyera chovala chake chauneneri.+

  • Zekariya 13:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Zikadzatero, aneneri azidzachita manyazi pa tsiku limenelo.+ Azidzachita manyazi ndi masomphenya awo pamene akulosera. Sadzavalanso chovala chapadera chaubweya+ kuti anamize anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena