2 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa m’chiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe.” Mateyu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yohane ameneyu, anali kuvala chovala chaubweya wa ngamila+ ndi lamba wachikopa+ m’chiuno mwake. Chakudya chake chinali dzombe+ ndi uchi.+
8 Iwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa m’chiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe.”
4 Koma Yohane ameneyu, anali kuvala chovala chaubweya wa ngamila+ ndi lamba wachikopa+ m’chiuno mwake. Chakudya chake chinali dzombe+ ndi uchi.+